Yeremiya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwana wamkazi wa Ziyoni* akufanana ndi mkazi wokongola komanso wosasatitsidwa.+ Yeremiya 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga,Vala chiguduli+ ndipo ugubuduke mʼphulusa. Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo, ulire mowawidwa mtima,+Chifukwa wowononga adzatiukira modzidzimutsa.+
26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga,Vala chiguduli+ ndipo ugubuduke mʼphulusa. Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo, ulire mowawidwa mtima,+Chifukwa wowononga adzatiukira modzidzimutsa.+