Yeremiya 52:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri ndi alonda atatu apakhomo.+ Yeremiya 52:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila+ mʼdziko la Hamati. Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+
24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri ndi alonda atatu apakhomo.+
27 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila+ mʼdziko la Hamati. Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+