7 Makolo athu ku Iguputo, sanayamikire ntchito zanu zodabwitsa.
Sanakumbukire chikondi chanu chokhulupirika chomwe ndi chochuluka,
Koma anapanduka panyanja, pafupi ndi Nyanja Yofiira.+
8 Koma Mulungu anawapulumutsa kuti dzina lake lilemekezedwe,+
Kuti mphamvu zake zidziwike.+