Ezekieli 20:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kumeneko mudzakumbukira khalidwe lanu ndi zonse zomwe munkachita nʼkudziipitsa nazo+ ndipo mudzanyansidwa chifukwa cha zoipa zonse zimene munachita.+ Ezekieli 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pa nthawiyo mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino. Mudzadzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu komanso zinthu zonyansa zimene munkachita.+
43 Kumeneko mudzakumbukira khalidwe lanu ndi zonse zomwe munkachita nʼkudziipitsa nazo+ ndipo mudzanyansidwa chifukwa cha zoipa zonse zimene munachita.+
31 Pa nthawiyo mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino. Mudzadzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu komanso zinthu zonyansa zimene munkachita.+