-
Zekariya 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndinauza makolo anu malamulo oti azitsatira ndipo ndinatumiza atumiki anga aneneri kuti akawachenjeze zimene zidzawachitikire ngati sangatsatire malamulowo. Kodi zonse zimene ndinanena kuti zidzawachitikirazo sizinawachitikire?’+ Choncho iwo anabwerera kwa ine nʼkunena kuti: ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba watichitira zimene anakonza mogwirizana ndi njira zathu ndi zochita zathu.’”+
-