-
Danieli 9:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Aisiraeli onse aphwanya Chilamulo chanu ndipo apatuka posamvera mawu anu. Choncho inu mwatitsanulira temberero ndi malumbiro amene analembedwa mʼChilamulo cha Mose, mtumiki wanu,+ chifukwa takuchimwirani. 12 Inu mwachitadi zimene munachenjeza kuti mudzachitira ifeyo+ ndi atsogoleri athu amene ankatilamulira.* Mwachita zimenezi potigwetsera tsoka lalikulu. Zimene zachitika mu Yerusalemu sizinayambe zachitikapo padziko lonse lapansi.+
-