Zekariya 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Pa tsiku limenelo, a mʼnyumba ya Davide ndi anthu okhala mu Yerusalemu adzawakumbira chitsime kuti ayeretsedwe ku machimo awo.”+ Zekariya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa tsikulo madzi amoyo+ adzatuluka mu Yerusalemu.+ Hafu ya madziwo idzapita kunyanja yakumʼmawa*+ ndipo hafu inayo idzapita kunyanja ya kumadzulo.*+ Zimenezi zidzachitika mʼnyengo yotentha ndiponso mʼnyengo yozizira. Chivumbulutso 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawankhosa.+
13 “Pa tsiku limenelo, a mʼnyumba ya Davide ndi anthu okhala mu Yerusalemu adzawakumbira chitsime kuti ayeretsedwe ku machimo awo.”+
8 Pa tsikulo madzi amoyo+ adzatuluka mu Yerusalemu.+ Hafu ya madziwo idzapita kunyanja yakumʼmawa*+ ndipo hafu inayo idzapita kunyanja ya kumadzulo.*+ Zimenezi zidzachitika mʼnyengo yotentha ndiponso mʼnyengo yozizira.
22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawankhosa.+