Salimo 107:33, 34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amasandutsa mitsinje kukhala chipululu,Ndiponso akasupe a madzi kukhala malo ouma.+34 Nthaka yobala zipatso amaisandutsa dziko lopanda chonde,+Chifukwa cha kuipa kwa anthu okhala mmenemo. Yeremiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mofanana ndi chitsime chimene chimatulutsa madzi ozizira,Yerusalemu amatulutsanso zinthu zoipa. Mkati mwake mukumveka phokoso la chiwawa komanso kuponderezana.+Nthawi zonse ndimaona matenda ndi miliri mumzindawo.
33 Amasandutsa mitsinje kukhala chipululu,Ndiponso akasupe a madzi kukhala malo ouma.+34 Nthaka yobala zipatso amaisandutsa dziko lopanda chonde,+Chifukwa cha kuipa kwa anthu okhala mmenemo.
7 Mofanana ndi chitsime chimene chimatulutsa madzi ozizira,Yerusalemu amatulutsanso zinthu zoipa. Mkati mwake mukumveka phokoso la chiwawa komanso kuponderezana.+Nthawi zonse ndimaona matenda ndi miliri mumzindawo.