6 Manase anatentha ana ake aamuna pamoto+ mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu,+ ankachita zamatsenga,+ ankawombeza, ankachita zanyanga ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu ndi olosera zamʼtsogolo.+ Iye anachita zinthu zoipa kwambiri pamaso pa Yehova ndipo anamukwiyitsa.