Yesaya 3:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uzani anthu olungama kuti zidzawayendera bwino,Iwo adzalandira mphoto chifukwa cha zimene akuchita.*+ 11 Tsoka kwa munthu woipa! Iye adzakumana ndi mavuto aakulu,Chifukwa zimene anachitira ena ndi manja ake, nayenso adzamuchitira zomwezo. Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musadzinamize, Mulungu sapusitsika. Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
10 Uzani anthu olungama kuti zidzawayendera bwino,Iwo adzalandira mphoto chifukwa cha zimene akuchita.*+ 11 Tsoka kwa munthu woipa! Iye adzakumana ndi mavuto aakulu,Chifukwa zimene anachitira ena ndi manja ake, nayenso adzamuchitira zomwezo.