-
1 Mafumu 21:25, 26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Palibenso munthu wina amene anatsimikiza mumtima mwake kuchita zoipa pamaso pa Yehova ngati Ahabu.+ Mkazi wake Yezebeli anamulimbikitsa kuchita zimenezo.+ 26 Ahabu anachita zinthu zonyansa kwambiri polambira mafano onyansa* ngati mmene Aamori onse anachitira, amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli.’”+
-