Mika 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo,Ndidzasonkhanitsa anthu amene ankayenda motsimphina.Ndidzasonkhanitsanso anthu amene anamwazikana,+Komanso anthu amene ndinawalanga. Mateyu 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye anayankha kuti: “Ine sananditumize kwa wina aliyense koma kwa nkhosa zotayika za nyumba ya Isiraeli.”+ Luka 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ndi ndani pakati panu amene atakhala ndi nkhosa 100, imodzi nʼkusowa, sangasiye nkhosa 99 zinazo mʼchipululu nʼkupita kukafunafuna imodzi imene yasowayo mpaka ataipeza?+
6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo,Ndidzasonkhanitsa anthu amene ankayenda motsimphina.Ndidzasonkhanitsanso anthu amene anamwazikana,+Komanso anthu amene ndinawalanga.
24 Iye anayankha kuti: “Ine sananditumize kwa wina aliyense koma kwa nkhosa zotayika za nyumba ya Isiraeli.”+
4 “Ndi ndani pakati panu amene atakhala ndi nkhosa 100, imodzi nʼkusowa, sangasiye nkhosa 99 zinazo mʼchipululu nʼkupita kukafunafuna imodzi imene yasowayo mpaka ataipeza?+