-
1 Mafumu 8:49, 50Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 inuyo, kumwamba kumene mumakhalako,+ mumve pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo ndipo muonetsetse kuti chilungamo chachitika kwa iwo. 50 Mukhululukire anthu anu amene anakuchimwirani. Muwakhululukire zimene anakulakwirani. Muchititse kuti adani awo amene anawatenga azikhudzidwa mtima ndipo aziwamvera chisoni,+
-