-
Danieli 2:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Akasidiwo anayankha mfumuyo kuti: “Palibe munthu padziko lapansi amene angathe kuchita zimene inu mfumu mukufuna. Palibe mfumu yaikulu kapena bwanamkubwa amene anauzapo wansembe wochita zamatsenga, munthu wolankhula ndi mizimu kapena Mkasidi kuti achite zimenezi. 11 Zimene inu mfumu mukufuna kuti tichite ndi zovuta, ndipo palibe munthu amene angakuuzeni maloto anu kupatulapo milungu, imene sikhala pakati pa anthu.”
-