10 Mizinda yanu yoyera yasanduka chipululu.
Ziyoni wasanduka chipululu,
Ndipo Yerusalemu wasanduka bwinja.+
11 Nyumba yathu yoyera ndiponso yaulemerero,
Imene makolo athu ankakutamandiranimo,
Yawotchedwa ndi moto,+
Ndipo zinthu zathu zonse zimene tinkaziona kuti ndi zamtengo wapatali zasanduka mabwinja