Salimo 79:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa mʼdziko limene ndi cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Yerusalemu amusandutsa bwinja.+ Maliro 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Misewu yopita ku Ziyoni ikulira chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+ Mageti ake onse awonongedwa.+ Ansembe ake akuusa moyo. Anamwali* ake agwidwa ndi chisoni ndipo iyeyo akumva ululu mumtima. Maliro 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa cha Phiri la Ziyoni limene lakhala bwinja+ ndipo tsopano nkhandwe zikuyendayenda mmenemo. Mika 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho chifukwa cha anthu inu,Ziyoni adzalimidwa ngati munda,Yerusalemu adzakhala mabwinja.+Ndipo phiri la nyumba* ya Mulungu lidzakhala ngati zitunda zamunkhalango.+
79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa mʼdziko limene ndi cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Yerusalemu amusandutsa bwinja.+
4 Misewu yopita ku Ziyoni ikulira chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+ Mageti ake onse awonongedwa.+ Ansembe ake akuusa moyo. Anamwali* ake agwidwa ndi chisoni ndipo iyeyo akumva ululu mumtima.
18 Chifukwa cha Phiri la Ziyoni limene lakhala bwinja+ ndipo tsopano nkhandwe zikuyendayenda mmenemo.
12 Choncho chifukwa cha anthu inu,Ziyoni adzalimidwa ngati munda,Yerusalemu adzakhala mabwinja.+Ndipo phiri la nyumba* ya Mulungu lidzakhala ngati zitunda zamunkhalango.+