Danieli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikupitiriza kuyangʼana, ndinaona mbuzi yamphongo+ ikuchokera kumadzulo* kudutsa padziko lonse lapansi koma sinkaponda pansi. Pakati pa maso a mbuziyo panali nyanga yoonekera patali.+ Danieli 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+
5 Ndikupitiriza kuyangʼana, ndinaona mbuzi yamphongo+ ikuchokera kumadzulo* kudutsa padziko lonse lapansi koma sinkaponda pansi. Pakati pa maso a mbuziyo panali nyanga yoonekera patali.+
21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+