2 Mafumu 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼchaka cha 38 cha Azariya+ mfumu ya Yuda, Zekariya+ mwana wa Yerobowamu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya ndipo analamulira miyezi 6. 2 Mafumu 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Salumu mwana wa Yabesi anakonzera chiwembu Zekariya nʼkumupha+ ku Ibuleamu+ ndipo iye anakhala mfumu mʼmalo mwake. 2 Mafumu 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Menahemu mwana wa Gadai, anachoka ku Tiriza+ kupita ku Samariya nʼkukapha Salumu+ mwana wa Yabesi ku Samariyako. Kenako iye anakhala mfumu mʼmalo mwake.
8 Mʼchaka cha 38 cha Azariya+ mfumu ya Yuda, Zekariya+ mwana wa Yerobowamu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya ndipo analamulira miyezi 6.
10 Ndiyeno Salumu mwana wa Yabesi anakonzera chiwembu Zekariya nʼkumupha+ ku Ibuleamu+ ndipo iye anakhala mfumu mʼmalo mwake.
14 Ndiyeno Menahemu mwana wa Gadai, anachoka ku Tiriza+ kupita ku Samariya nʼkukapha Salumu+ mwana wa Yabesi ku Samariyako. Kenako iye anakhala mfumu mʼmalo mwake.