11 Pa tsiku limene unangoima nʼkumaonerera,
Pa tsiku limene adani anagwira gulu la asilikali a mʼbale wako nʼkupita nawo ku ukapolo,+
Ndiponso pamene anthu akudziko lina analowa mumzinda wake nʼkuchita maere+ pa Yerusalemu,
Iwe unali ngati mmodzi wa adaniwo.