Yesaya 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwina Yehova Mulungu wanu amva mawu a Rabisake, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamutuma kuti adzanyoze Mulungu wamoyo.+ Ndipo amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva. Choncho inuyo mupemphere+ mʼmalo mwa anthu amene atsala.’”+
4 Mwina Yehova Mulungu wanu amva mawu a Rabisake, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamutuma kuti adzanyoze Mulungu wamoyo.+ Ndipo amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva. Choncho inuyo mupemphere+ mʼmalo mwa anthu amene atsala.’”+