Yesaya 45:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa ndi Yehova ndipo chipulumutso chake chidzakhala chosatha.+ Inu simudzachititsidwa manyazi kapena kunyozeka mpaka kalekale.+ Yesaya 54:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usachite mantha,+ chifukwa sudzachititsidwa manyazi.+Usachite manyazi, chifukwa sudzakhumudwitsidwa. Iwe udzaiwala manyazi apaubwana wako,Ndipo sudzakumbukiranso kunyozeka kwa paumasiye wako.
17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa ndi Yehova ndipo chipulumutso chake chidzakhala chosatha.+ Inu simudzachititsidwa manyazi kapena kunyozeka mpaka kalekale.+
4 Usachite mantha,+ chifukwa sudzachititsidwa manyazi.+Usachite manyazi, chifukwa sudzakhumudwitsidwa. Iwe udzaiwala manyazi apaubwana wako,Ndipo sudzakumbukiranso kunyozeka kwa paumasiye wako.