Maliro 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Misewu yopita ku Ziyoni ikulira chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+ Mageti ake onse awonongedwa.+ Ansembe ake akuusa moyo. Anamwali* ake agwidwa ndi chisoni ndipo iyeyo akumva ululu mumtima. Maliro 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye wapasula msasa wake+ ngati chisimba chamʼmunda. Iye wathetsa zikondwerero zake.+ Yehova wachititsa kuti zikondwerero ndi sabata ziiwalike mu Ziyoni,Ndipo chifukwa cha mkwiyo wake waukulu sakuganiziranso za mfumu ndi wansembe.+
4 Misewu yopita ku Ziyoni ikulira chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+ Mageti ake onse awonongedwa.+ Ansembe ake akuusa moyo. Anamwali* ake agwidwa ndi chisoni ndipo iyeyo akumva ululu mumtima.
6 Iye wapasula msasa wake+ ngati chisimba chamʼmunda. Iye wathetsa zikondwerero zake.+ Yehova wachititsa kuti zikondwerero ndi sabata ziiwalike mu Ziyoni,Ndipo chifukwa cha mkwiyo wake waukulu sakuganiziranso za mfumu ndi wansembe.+