Zekariya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.