45 Davide anayankha Mfilisitiyo kuti: “Iwe ukubwera kudzamenyana ndi ine ndi lupanga, mkondo ndi nthungo,+ koma ine ndikubwera kudzamenyana nawe mʼdzina la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ Mulungu wa asilikali a Isiraeli, amene iweyo wamunyoza.+