Yesaya 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzakupatsani chilango,Ndidzakuyengani nʼkuchotseratu zonyansa zanu zonse,Ndidzachotsa zinthu zonse zimene zikuchititsa kuti musakhale oyera.+ Yeremiya 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ‘Ngakhale utasambira soda ndiponso sopo wambiri,Zolakwa zako ndidzazionabe ngati zinthu zothimbirira,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
25 Ndidzakupatsani chilango,Ndidzakuyengani nʼkuchotseratu zonyansa zanu zonse,Ndidzachotsa zinthu zonse zimene zikuchititsa kuti musakhale oyera.+
22 ‘Ngakhale utasambira soda ndiponso sopo wambiri,Zolakwa zako ndidzazionabe ngati zinthu zothimbirira,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.