Yesaya 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzakutembenuzirani dzanja langa. Ndidzasungunula zonyansa zanu zonse, ndipo ndidzachotsa nyansi zanu zonse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:25 Yesaya 1, ptsa. 32-33
25 Ndidzakutembenuzirani dzanja langa. Ndidzasungunula zonyansa zanu zonse, ndipo ndidzachotsa nyansi zanu zonse.+