Maliko 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anawauzanso kuti: “Nyale saivindikira ndi dengu* kapena kuiika pansi pa bedi, amatero ngati? Koma amaiika pachoikapo nyale,+ si choncho kodi? Luka 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Munthu akayatsa nyale saiika pamalo obisika kapena kuivindikira ndi dengu,* koma amaiika pachoikapo nyale,+ kuti amene akulowa aone kuwala.
21 Iye anawauzanso kuti: “Nyale saivindikira ndi dengu* kapena kuiika pansi pa bedi, amatero ngati? Koma amaiika pachoikapo nyale,+ si choncho kodi?
33 Munthu akayatsa nyale saiika pamalo obisika kapena kuivindikira ndi dengu,* koma amaiika pachoikapo nyale,+ kuti amene akulowa aone kuwala.