Mateyu 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu akayatsa nyale saivindikira ndi dengu, koma amaiika pachoikapo nyale ndipo imaunikira onse mʼnyumbamo.+ Maliko 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anawauzanso kuti: “Nyale saivindikira ndi dengu* kapena kuiika pansi pa bedi, amatero ngati? Koma amaiika pachoikapo nyale,+ si choncho kodi? Luka 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe amene amati akayatsa nyale, amaivindikira ndi chiwiya kapena kuiika pansi pa bedi. Koma amaiika pachoikapo nyale kuti amene akulowa aone kuwala.+
15 Anthu akayatsa nyale saivindikira ndi dengu, koma amaiika pachoikapo nyale ndipo imaunikira onse mʼnyumbamo.+
21 Iye anawauzanso kuti: “Nyale saivindikira ndi dengu* kapena kuiika pansi pa bedi, amatero ngati? Koma amaiika pachoikapo nyale,+ si choncho kodi?
16 Palibe amene amati akayatsa nyale, amaivindikira ndi chiwiya kapena kuiika pansi pa bedi. Koma amaiika pachoikapo nyale kuti amene akulowa aone kuwala.+