Ekisodo 21:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Wina akavulaza mnzake koopsa, pazikhala diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi,+ 25 kutentha ndi moto kulipira kutentha ndi moto, chilonda kulipira chilonda, kumenya kulipira kumenya. Levitiko 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuthyola fupa kulipira kuthyola fupa, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino. Mmene wavulazira mnzake nayenso muzimʼvulaza chimodzimodzi.+ Deuteronomo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musamamve* chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.”+
24 Wina akavulaza mnzake koopsa, pazikhala diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi,+ 25 kutentha ndi moto kulipira kutentha ndi moto, chilonda kulipira chilonda, kumenya kulipira kumenya.
20 Kuthyola fupa kulipira kuthyola fupa, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino. Mmene wavulazira mnzake nayenso muzimʼvulaza chimodzimodzi.+
21 Musamamve* chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.”+