25 Ndiyeno anawafunsa kuti: “Chikhulupiriro chanu chili kuti?” Koma iwo anagwidwa ndi mantha ndipo anathedwa nzeru, moti anayamba kufunsana kuti: “Kodi munthu ameneyu ndi ndani kwenikweni? Nanga taonani, akutha kulamula mphepo ndi madzi ndipo zikumumvera.”+