Luka 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine ndipo palibe amene akumudziwa bwino Mwana koma Atate okha. Komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha+ ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.”+ Yohane 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ngati mmene zilili kuti Atate amandidziwa ndipo inenso ndimadziwa Atate.+ Choncho ndikupereka moyo wanga chifukwa cha nkhosazo.+ 1 Yohane 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komabe, tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera padzikoli+ ndipo anatipatsa nzeru kuti tidziwe Mulungu woona. Kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu, ndife ogwirizana naye.+ Iyeyo ndi Mulungu woona ndipo amapereka moyo wosatha.+
22 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine ndipo palibe amene akumudziwa bwino Mwana koma Atate okha. Komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha+ ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.”+
15 ngati mmene zilili kuti Atate amandidziwa ndipo inenso ndimadziwa Atate.+ Choncho ndikupereka moyo wanga chifukwa cha nkhosazo.+
20 Komabe, tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera padzikoli+ ndipo anatipatsa nzeru kuti tidziwe Mulungu woona. Kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu, ndife ogwirizana naye.+ Iyeyo ndi Mulungu woona ndipo amapereka moyo wosatha.+