Maliko 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chifukwa aliyense amene akufuna kupulumutsa moyo wake adzautaya. Koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine ndi uthenga wabwino, adzaupulumutsa.+ Luka 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa aliyense amene akufuna kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma aliyense amene wataya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+ Luka 17:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Aliyense wofunitsitsa kuteteza moyo wake adzautaya, koma aliyense wotaya moyo wake adzausunga.+ Yohane 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aliyense amene amakonda moyo wake akuuwononga, koma aliyense amene amadana ndi moyo wake+ mʼdziko lino akuuteteza kuti adzapeze moyo wosatha.+ Chivumbulutso 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa+ ndiponso chifukwa cha uthenga umene ankalalikira+ ndipo anali okonzeka kufa.+
35 Chifukwa aliyense amene akufuna kupulumutsa moyo wake adzautaya. Koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine ndi uthenga wabwino, adzaupulumutsa.+
24 Chifukwa aliyense amene akufuna kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma aliyense amene wataya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+
25 Aliyense amene amakonda moyo wake akuuwononga, koma aliyense amene amadana ndi moyo wake+ mʼdziko lino akuuteteza kuti adzapeze moyo wosatha.+
11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa+ ndiponso chifukwa cha uthenga umene ankalalikira+ ndipo anali okonzeka kufa.+