-
Mateyu 15:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Ndiyeno Yesu anamuyankha kuti: “Mayi iwe, chikhulupiriro chako ndi chachikulu. Zimene ukufuna zichitike kwa iwe.” Ndipo nthawi yomweyo mwana wake anachira.
-