Mateyu 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yesu anauza kapitawo wa asilikaliyo kuti: “Pita. Malinga ndi chikhulupiriro chako, chimene ukufuna chichitike.”+ Mu ola lomwelo, wantchito uja anachira.
13 Kenako Yesu anauza kapitawo wa asilikaliyo kuti: “Pita. Malinga ndi chikhulupiriro chako, chimene ukufuna chichitike.”+ Mu ola lomwelo, wantchito uja anachira.