Maliko 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, zinthu zonse zimene mukupempha ndi kuzipempherera, muzikhulupirira kuti mwazilandira kale ndipo mudzazilandiradi.+ Luka 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho ndikukuuzani, pitirizani kupempha+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna ndipo mudzapeza. Pitirizani kugogoda ndipo adzakutsegulirani.+ Yohane 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso chilichonse chimene mudzapemphe mʼdzina langa, ine ndidzachichita, kuti Atate alemekezedwe kudzera mwa Mwana wake.+ Yakobo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru, azipempha kwa Mulungu+ ndipo adzamupatsa,+ chifukwa iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.*+ 1 Yohane 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo chilichonse chimene tingamupemphe adzatipatsa,+ chifukwa timamvera malamulo ake komanso tikuchita zinthu zomusangalatsa.
24 Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, zinthu zonse zimene mukupempha ndi kuzipempherera, muzikhulupirira kuti mwazilandira kale ndipo mudzazilandiradi.+
9 Choncho ndikukuuzani, pitirizani kupempha+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna ndipo mudzapeza. Pitirizani kugogoda ndipo adzakutsegulirani.+
13 Komanso chilichonse chimene mudzapemphe mʼdzina langa, ine ndidzachichita, kuti Atate alemekezedwe kudzera mwa Mwana wake.+
5 Choncho ngati wina akusowa nzeru, azipempha kwa Mulungu+ ndipo adzamupatsa,+ chifukwa iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.*+
22 Ndipo chilichonse chimene tingamupemphe adzatipatsa,+ chifukwa timamvera malamulo ake komanso tikuchita zinthu zomusangalatsa.