Machitidwe 4:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene Petulo ndi Yohane ankalankhula ndi anthuwo, ansembe, woyangʼanira kachisi ndiponso Asaduki+ anafika. 2 Iwo anakwiya chifukwa atumwiwo ankaphunzitsa anthu ndiponso kulalikira mosapita mʼmbali zoti Yesu anaukitsidwa.+ Machitidwe 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa Asaduki amanena kuti munthu wakufa sangauke komanso kulibe angelo kapena cholengedwa chauzimu. Pomwe Afarisi amavomereza poyera kuti zonsezi zilipo.+
4 Pamene Petulo ndi Yohane ankalankhula ndi anthuwo, ansembe, woyangʼanira kachisi ndiponso Asaduki+ anafika. 2 Iwo anakwiya chifukwa atumwiwo ankaphunzitsa anthu ndiponso kulalikira mosapita mʼmbali zoti Yesu anaukitsidwa.+
8 Chifukwa Asaduki amanena kuti munthu wakufa sangauke komanso kulibe angelo kapena cholengedwa chauzimu. Pomwe Afarisi amavomereza poyera kuti zonsezi zilipo.+