-
Luka 21:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Nthawi ina, pamene anthu ena ankalankhula za kachisi, mmene anamukongoletsera ndi miyala yabwino kwambiri komanso mphatso zoperekedwa kwa Mulungu,+ 6 iye ananena kuti: “Kunena za zinthu zimene mukuzionazi, masiku adzafika pamene sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+
-