Luka 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nthawi ina, anthu ena anali kulankhula za kachisi, mmene anam’kongoletsera ndi miyala yochititsa kaso komanso mphatso zoperekedwa kwa Mulungu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:5 Yesu—Ndi Njira, tsa. 255 Nsanja ya Olonda,3/1/1990, tsa. 25
5 Nthawi ina, anthu ena anali kulankhula za kachisi, mmene anam’kongoletsera ndi miyala yochititsa kaso komanso mphatso zoperekedwa kwa Mulungu.+