-
Mateyu 7:22, 23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pa tsiku limenelo ambiri adzandiuza kuti: ‘Ambuye, Ambuye,+ kodi ife sitinalosere mʼdzina lanu ndi kutulutsa ziwanda mʼdzina lanu ndiponso kuchita ntchito zambiri zamphamvu mʼdzina lanu?’+ 23 Koma ine ndidzawauza kuti: ‘Sindikukudziwani ngakhale pangʼono! Chokani pamaso panga, anthu osamvera malamulo inu.’+
-