Luka 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsiku lina iye akuphunzitsa, Afarisi ndi aphunzitsi a Chilamulo amene anachokera mʼmidzi yonse ya Galileya, ku Yudeya ndi ku Yerusalemu anakhala pansi pamalo omwewo. Ndipo mphamvu ya Yehova* inali pa iye kuti athe kuchiritsa.+ Luka 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Gulu lonse la anthulo linkayesetsa kuti limugwire, chifukwa mphamvu zinkatuluka mwa iye+ nʼkuchiritsa anthu onsewo.
17 Tsiku lina iye akuphunzitsa, Afarisi ndi aphunzitsi a Chilamulo amene anachokera mʼmidzi yonse ya Galileya, ku Yudeya ndi ku Yerusalemu anakhala pansi pamalo omwewo. Ndipo mphamvu ya Yehova* inali pa iye kuti athe kuchiritsa.+
19 Gulu lonse la anthulo linkayesetsa kuti limugwire, chifukwa mphamvu zinkatuluka mwa iye+ nʼkuchiritsa anthu onsewo.