Mateyu 8:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yesu, atalowa mʼnyumba mwa Petulo, anaona apongozi aakazi a Petulo+ ali chigonere, akudwala malungo.*+ 15 Choncho anagwira dzanja la mayiwo+ ndipo malungowo anatheratu, moti anadzuka nʼkuyamba kumutumikira. Luka 4:38, 39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Atatuluka mʼsunagogemo, anakalowa mʼnyumba ya Simoni. Pa nthawiyo apongozi aakazi a Simoni ankadwala malungo aakulu,* choncho anamupempha kuti awathandize.+ 39 Ndiyeno anaima pamene mayiwo anagona nʼkuwachiritsa ndipo malungowo anatheratu. Nthawi yomweyo mayiwo anadzuka nʼkuyamba kuwatumikira.
14 Tsopano Yesu, atalowa mʼnyumba mwa Petulo, anaona apongozi aakazi a Petulo+ ali chigonere, akudwala malungo.*+ 15 Choncho anagwira dzanja la mayiwo+ ndipo malungowo anatheratu, moti anadzuka nʼkuyamba kumutumikira.
38 Atatuluka mʼsunagogemo, anakalowa mʼnyumba ya Simoni. Pa nthawiyo apongozi aakazi a Simoni ankadwala malungo aakulu,* choncho anamupempha kuti awathandize.+ 39 Ndiyeno anaima pamene mayiwo anagona nʼkuwachiritsa ndipo malungowo anatheratu. Nthawi yomweyo mayiwo anadzuka nʼkuyamba kuwatumikira.