Maliko 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti Pasika+ ndi Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa+ zichitike. Ndipo ansembe aakulu ndi alembi ankafunafuna njira yoti agwiritse ntchito pogwira* Yesu mochenjera nʼkumupha.+ Luka 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alembi ndi ansembe aakulu aja atazindikira kuti mufanizolo akunena za iwowo, anayesetsa kupeza mpata kuti amugwire ola lomwelo, koma ankaopa anthu.+
14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti Pasika+ ndi Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa+ zichitike. Ndipo ansembe aakulu ndi alembi ankafunafuna njira yoti agwiritse ntchito pogwira* Yesu mochenjera nʼkumupha.+
19 Alembi ndi ansembe aakulu aja atazindikira kuti mufanizolo akunena za iwowo, anayesetsa kupeza mpata kuti amugwire ola lomwelo, koma ankaopa anthu.+