Maliko 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti pasika+ ndi chikondwerero+ cha mikate yopanda chofufumitsa zichitike.+ Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yogwirira Yesu mochenjera ndi kumupha.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 266 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, ptsa. 8-9
14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti pasika+ ndi chikondwerero+ cha mikate yopanda chofufumitsa zichitike.+ Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yogwirira Yesu mochenjera ndi kumupha.+