9 Koma anthu ena a mʼgulu lotchedwa Sunagoge wa Omasulidwa anafika limodzi ndi anthu ena a ku Kurene, a ku Alekizandiriya, ku Kilikiya ndiponso a ku Asia kudzatsutsana ndi Sitefano. 10 Koma iwo sanathe kulimbana ndi nzeru zake komanso mzimu woyera umene unkamutsogolera akamalankhula.+