-
Luka 22:31-33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Simoni, Simoni! Ndithu Satana akufuna kuti nonsenu akupeteni ngati tirigu.+ 32 Koma ine ndakupempherera kuti chikhulupiriro chako chisathe.+ Choncho iwenso ukabwerera, ukalimbikitse abale ako.”+ 33 Kenako iye anauza Yesu kuti: “Ambuye, ndine wokonzeka kupita nanu limodzi kundende kapena kufa nanu limodzi.”+
-