Mateyu 5:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anayamba kuwaphunzitsa kuti: 3 “Osangalala ndi anthu amene amazindikira zosowa zawo zauzimu+ chifukwa Ufumu wakumwamba ndi wawo. Yakobo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tamverani abale anga okondedwa. Kodi Mulungu sanasankhe anthu amene dzikoli limawaona kuti ndi osauka kuti akhale olemera mʼchikhulupiriro+ komanso kuti akhale oyenera kupatsidwa Ufumu umene Mulungu analonjeza anthu amene amamukonda?+
2 Kenako anayamba kuwaphunzitsa kuti: 3 “Osangalala ndi anthu amene amazindikira zosowa zawo zauzimu+ chifukwa Ufumu wakumwamba ndi wawo.
5 Tamverani abale anga okondedwa. Kodi Mulungu sanasankhe anthu amene dzikoli limawaona kuti ndi osauka kuti akhale olemera mʼchikhulupiriro+ komanso kuti akhale oyenera kupatsidwa Ufumu umene Mulungu analonjeza anthu amene amamukonda?+