Yesaya 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Yehova akupatsani chizindikiro: Tamverani! Mtsikana* adzakhala woyembekezera ndipo adzabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo adzamʼpatsa dzina lakuti Emanueli.*+ Mateyu 1:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Yosefe anadzuka nʼkuchita mogwirizana ndi zimene mngelo wa Yehova* anamuuza. Anatenga mkazi wake nʼkupita naye kunyumba. 25 Koma sanagone naye mpaka anabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Yesu.+
14 Choncho Yehova akupatsani chizindikiro: Tamverani! Mtsikana* adzakhala woyembekezera ndipo adzabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo adzamʼpatsa dzina lakuti Emanueli.*+
24 Ndiyeno Yosefe anadzuka nʼkuchita mogwirizana ndi zimene mngelo wa Yehova* anamuuza. Anatenga mkazi wake nʼkupita naye kunyumba. 25 Koma sanagone naye mpaka anabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Yesu.+