Maliko 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo mukaimirira nʼkumapemphera, muzikhululuka chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireninso machimo anu.”+ Aefeso 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma muzikomerana mtima, muzisonyezana chifundo chachikulu+ komanso muzikhululukirana ndi mtima wonse, ngati mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+ Akolose 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pitirizani kulolerana ndi kukhululukirana ndi mtima wonse,+ ngakhale pamene wina ali ndi chifukwa chodandaulira za mnzake.+ Mofanana ndi Yehova* amene anakukhululukirani ndi mtima wonse, inunso muzichita chimodzimodzi.+
25 Ndipo mukaimirira nʼkumapemphera, muzikhululuka chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireninso machimo anu.”+
32 Koma muzikomerana mtima, muzisonyezana chifundo chachikulu+ komanso muzikhululukirana ndi mtima wonse, ngati mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+
13 Pitirizani kulolerana ndi kukhululukirana ndi mtima wonse,+ ngakhale pamene wina ali ndi chifukwa chodandaulira za mnzake.+ Mofanana ndi Yehova* amene anakukhululukirani ndi mtima wonse, inunso muzichita chimodzimodzi.+