Akolose 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho monga anthu osankhidwa ndi Mulungu,+ oyera ndi okondedwa, valani chifundo chachikulu,+ kukoma mtima, kudzichepetsa,+ kufatsa+ komanso kuleza mtima.+ 1 Petulo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pomaliza, nonsenu mukhale amaganizo amodzi,+ muzimverana chisoni, muzikonda abale, mukhale ndi chifundo chachikulu+ ndiponso mukhale odzichepetsa.+
12 Choncho monga anthu osankhidwa ndi Mulungu,+ oyera ndi okondedwa, valani chifundo chachikulu,+ kukoma mtima, kudzichepetsa,+ kufatsa+ komanso kuleza mtima.+
8 Pomaliza, nonsenu mukhale amaganizo amodzi,+ muzimverana chisoni, muzikonda abale, mukhale ndi chifundo chachikulu+ ndiponso mukhale odzichepetsa.+