4 Koma popeza kuti Mulungu ndi wachifundo chochuluka,+ komanso chifukwa cha chikondi chake chachikulu chimene anatisonyeza,+ 5 anapangitsa kuti tikhale amoyo limodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa chifukwa cha machimo athu,+ ndipotu inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu.